Luke 19:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Poona zimenezi, anthu onse adayamba kung'ung'udza. Adati, “Wakakhala kunyumba kwa munthu wochimwa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene anachiona anadandaula onse, nanena, Analowa amchereze munthu ali wochimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse ataona zimenezi anayamba kungʼungʼudza, nati, “Iye akupita kuti akakhale mlendo wa wochimwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene anaciona anadandaula onse, nanena, Analowa amcereze munthu ali wocimwa.