Luke 2:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Simeoni adalandira mwanayo m'manja mwake, nayamba kutamanda Mulungu ndi mau akuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pomwepo iye anamlandira Iye m'manja mwake, nalemekeza Mulungu, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Simeoni anamunyamula mʼmanja mwake nayamika Mulungu, nati:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pomwepo iye anamlandira iye m'manja mwace, nalemekeza Mulungu, nati,