Luke 2:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwapereka kuŵala kodzaunikira anthu a mitundu ina, kodzakhala ulemerero wa anthu anu Aisraele.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuunika kukhale chivumbulutso cha kwa anthu a mitundu, ndi ulemerero wa anthu anu Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuwala kowunikira anthu a mitundu ina ndi kwa ulemerero kwa anthu anu Aisraeli.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuunika kukhale cibvumbulutso ca kwa anthu a mitundu, Ndi ulemerero wa anthu anu Israyeli.