Luke 2:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atate ndi amai a mwanayo ankangodabwa nazo zimene Simeoni ankanena za mwanayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atate ndi amake anali kuzizwa ndi zinthu zolankhulidwa za Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abambo ndi amayi a Mwanayo anadabwa chifukwa cha zimene zinanenedwa za Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atate ndi amace anali kuzizwa ndi zinthu zolankhulidwa za iye.