Luke 2:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yesu anali ndi zaka khumi ndi ziŵiri, iwo adapita kumeneko monga adaazoloŵera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Iye anakhala ndi zaka zake khumi ndi ziwiri, anakwera iwo monga machitidwe a chikondwerero;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ali ndi zaka khumi ndi ziwiri, anapita ku phwando, monga mwa mwambo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene iye anakhala ndi zaka zace khumi ndi ziwiri, anakwera iwo monga macitidwe a phwando;