Luke 2:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapita kukalembedwa pamodzi ndi Maria, mkazi wake, amene anali ndi pathupi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kukalembedwa iye mwini pamodzi ndi Maria, wopalidwa naye ubwenzi; ndi uyu anali ndi pakati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapita kumeneko kukalembetsa pamodzi ndi Mariya, amene anapalana naye ubwenzi kuti akwatirane ndipo anali woyembekezera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kukalembedwa iye mwini pamodzi ndi Mariya, wopalidwa naye ubwenzi; ndi uyu anali ndi pakati,