Luke 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anali kumeneko, nthaŵi yake yoti Maria achire idakwana,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali pokhala iwo komweko, masiku ake a kubala anakwanira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ali kumeneko, nthawi inakwana yakuti mwana abadwe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali pokhaia iwo komweko, masiku ace a kubala anakwanira.