Luke 20:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatumanso wachitatu, koma uyunso alimiwo adamuvulaza, namtaya kunja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatumizanso wina wachitatu; ndipo iyenso anamlasa, namtaya kunja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatumizanso wina wachitatu ndipo iwo anamuvulaza namuponya kunja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatumizanso wina wacitatu; ndipo iyenso anamlasa, namtaya kunja.