Luke 20:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu adzabwera naŵapha alimiwo, munda uja nkuubwereka ena.” Anthu aja atamva zimenezi adati, “Ai, msatero.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye adzafika nadzaononga olima munda aja, nadzapatsa munda kwa ena. Ndipo pamene iwo anamva, anati, Musatero iai!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzabwera ndi kupha alimi aja ndi kupereka mundawo kwa ena.” Pamene anthu anamva izi, anati, “Musatero ayi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iye adzafika nadzaononga olima munda aja, nadzapatsa munda kwa ena. Ndipo pamene iwo anamva, anati, Musatero iail