Luke 20:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
namufunsa kuti, “Mutiwuze, kodi mphamvu zoti muzichita zimenezi mudazitenga kuti? Kaya ndani adakupatsani mphamvu zimenezi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anati, nanena naye, Mutiuze muchita izi ndi ulamuliro wotani? Kapena ndani iye amene anakupatsani ulamuliro umene?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati, “Mutiwuze mukuchita izi ndi ulamuliro wayani? Ndani anakupatsani ulamuliro uwu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anati, nanena naye, Mutiuze mucita in ndi ulamuliro wotani? Kapena ndani iye amene anakupatsani ulamuliro umene?