Luke 20:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tandiwonetsani ndalama. Kodi ili ndi nkhope ya yani, ndipo ili ndi dzina la yani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tandionetsani Ine rupiya latheka. Chithunzithunzi ndi cholemba chake ncha yani? Anati iwo, Cha Kaisara.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Onetseni ndalama. Chithunzi ndi malembawa ndi zayani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tandionetsani Ine rupiya latheka. Cithunzithunzi ndi colemba cace nca yani? Anati iwo, Ca Kaisara.