Luke 20:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adalephera kumutapa m'kamwa pamaso pa anthu pa zimene Iye adalankhula. Iwo adathedwa nzeru ndi zimene Yesu adaayankha, nkungoti chete.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo sanakhoze kugwira mauwo pamaso pa anthu; ndipo anazizwa ndi kuyankha kwake, nakhala chete.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo analephera kumupeza cholakwa pa zimene ankayankhula pamaso pa anthu. Ndipo pothedwa nzeru ndi yankho lake, iwo anakhala chete.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sanakhoza kugwira mauwo pamaso pa anthu; ndipo anazizwa ndi kuyankha kwace, nakhala cete.