Luke 20:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono padaali anthu asanu ndi aŵiri pachibale pao. Woyamba adaakwatira mkazi, koma adamwalira osamsiyira mwana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono panali abale asanu ndi awiri; ndipo woyamba anakwatira mkazi, nafa wopanda mwana;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano panali abale asanu ndi awiri. Woyambayo anakwatira mkazi ndipo anafa wopanda mwana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono panali abale asanu ndi awiri; ndipo woyamba anakwatira mkazi, nafa wopanda mwana;