Luke 20:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo wachitatu nayenso adaloŵa chokolo. Onse aja asanu ndi aŵiri adachita chimodzimodzi, koma onse adamwalira osamsiyira ana mkaziyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi wachitatu anamtenga mkaziyo; ndipo choteronso asanu ndi awiri onse, sanasiye mwana, namwalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo kenaka wachitatuyo anamukwatira iye, ndipo chimodzimodzi asanu ndi awiri aja anafa osasiya ana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi wacitatu anamtenga mkaziyo; ndipo coteronso asanu ndi awiri onse, sanasiya mwana, namwalira.