Luke 20:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kodi Yohane Mbatizi kuti azibatiza, mphamvu zake adaazitenga kwa yani, kwa Mulungu kapena kwa anthu?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ubatizo wa Yohane unachokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Kodi ubatizo wa Yohane, unali wochokera kumwamba, kapena wochokera kwa anthu?’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ubatizo wa Yohane unacokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu?