Luke 20:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adaŵafunsa kuti, “Kodi inu, bwanji amati Mpulumutsi wolonjezedwa uja ndi mwana wa Davide?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Iye anati kwa iwo, Amanena bwanji kuti Khristuyo ndiye mwana wa Davide?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yesu anawawuza kuti, “Zikutheka bwanji kuti aziti Khristu ndi mwana wa Davide?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye anati kwa iwo, Amanena bwanji kuti Kristuyo ndiye mwana wa Davine?