Luke 20:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Davide yemwe m'buku la Masalimo akuti, “ ‘Chauta adauza Mbuye wanga kuti: Khala ku dzanja langa lamanja
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Davide yekha anena m'buku la Masalmo, Ambuye ananena kwa Ambuye wanga, ukhale pa dzanja langa lamanja,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide mwini wake akunenetsa mʼbuku la Masalimo kuti, “Ambuye anati kwa Ambuye anga: ‘Khalani ku dzanja langa lamanja,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Davine yekha anena m'buku la Masalmo, Ambuye ananena kwa Ambuye wanga, Ukhale pa dzanja langa lamanja,