Luke 20:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Davide akutchula Mpulumutsi wolonjezedwa uja kuti Mbuye wake. Tsono angakhale mwana wakenso bwanji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chotero Davide anamtchula Iye Ambuye, ndipo nanga ali mwana wake bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide akumutcha Iye ‘Ambuye.’ Nanga zingatheke bwanji kuti Iye akhale mwana wake?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cotero Davine anamchula iye Ambuye, ndipo nanga ali mwana wace bwanji?