Luke 20:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anthu onse ankamvetsera zimene Yesu ankalankhula, Iye adauza ophunzira ake kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anthu onse analinkumva Iye, anati kwa ophunzira,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anthu onse ankamvetsera, Yesu anati kwa ophunzira ake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anthu onse anallinkumva iye, anati kwa ophunzira,