Luke 21:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha Ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse adzadana ndi inu chifukwa cha dzina langa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse adzakudani chifukwa cha Ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse adzadana ndi inu cifukwa ca dzina langa.