Luke 21:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa masiku amenewo adzakhala masiku akulipsira, kuti zonse zija zimene zidaalembedwa m'Malembo zipherezere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa amenewa ndi masiku akubwezera, kuti zonse zidalembedwa zichitike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti iyi ndi nthawi yachilango pokwaniritsa zonse zimene zinalembedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa amenewa ndi masiku akubwezera, kuti zonse zidalembedwa zicitike.