Luke 21:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukamaona kuti masamba akuphuka, mumadziŵa kuti chilimwe chayandikira kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamene iphukira, muipenya nimuzindikira pa nokha kuti dzinja lili pafupi pomwepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ikamatulutsa masamba, mumakhoza kudzionera nokha ndi kudziwa kuti dzinja lili pafupi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamene iphukira, muipenya nimuzindikira pa nokha kuti dzinja liri pafupi pomwepo.