Luke 21:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu ndikunenetsa kuti zonsezi zidzaoneka anthu a mbadwo unoŵa asanamwalire onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Indetu ndinena ndinu, Mbadwo uno sudzapitirira, kufikira zonse zitachitika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti mʼbado uno sudzatha mpaka zinthu zonsezi zitachitika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Indetu ndinena ndinu, Mbadwo uno sudzapitirira, kufikira zonse zitacitika.