Luke 21:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu lidzaŵagwera ngati msampha anthu onse okhala pa dziko lonse lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti lidzatero ndi kufikira anthu onse akukhala pankhope pa dziko lonse lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti lidzafika pa onse okhala pa dziko lonse lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti Iidzatero ndi kufikira anthu onse akukhala pankhope pa dziko lonse lapansi.