Luke 21:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anthu onse ankalaŵirira m'mamaŵa kubwera kwa Iye ku Nyumba ya Mulungu kudzamva mau ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse analawira mamawa kudza kwa Iye ku Kachisi kudzamvera Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anthu onse amabwera mmamawa kudzamumva Iye ku Nyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse analawira mamawa kudza kwa iye kuKacisi kudzamvera Iye.