Luke 22:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma ndithudi wondipereka kwa adani akudya nane pamodzi pompano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma onani, dzanja lake la iye amene adzandipereka ali pagome pano pamodzi ndi Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma dzanja la amene akundipereka Ine lili pamodzi ndi langa pa chakudya pano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma onani, dzanja lace la iye amene adzandipereka ali pagome pano pamodzi ndi Ine.