Luke 22:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo onse adayamba kumafunsana kuti, “Kodi ndani mwa ife angachite zotere?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayamba kufunsana mwa iwo okha, ndiye yani mwa iwo amene adzachita ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayamba kufunsana pakati pawo kuti ndi ndani wa iwo amene akanachita ichi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayamba kufunsana mwa iwo okha, ndiye yani mwa iwo amene adzacita ici.