Luke 22:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ophunzira aja adayamba kutsutsana kuti, “Kodi mwa ife amati wamkulu ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunakhala kutsutsana mwa iwo, ndani wa iwo ayesedwe wamkulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso mkangano unabuka pakati pawo kuti ndani mwa iwo amene amaganiziridwa kukhala wamkulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunakhala kutsutsana mwa iwo, ndani wa iwo ayesedwe wamkuru.