Luke 22:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ophunzirawo adati, “Ambuye, aŵa malupanga, tili nawo kale aŵiri.” Yesu adaŵauza kuti, “Chabwino, basi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo anati, Ambuye, taonani, malupanga awiri siwa. Ndipo anati kwa iwo, Chakwanira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ophunzira anati, “Taonani Ambuye, awa malupanga awiri.” Iye anayankha kuti, “Amenewa akwanira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo anati, Ambuye, taonani, malupanga awir siwa. Ndipo anati kwa iwo, Cakwa nira.