Luke 22:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adapatukana nawo kadera, kutalika kwake ngati pamene mwala ungafike munthu atauponya. Apo adagwada pansi nayamba kupemphera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapatukana nao kutalika kwake ngati kuponya mwala, nagwada pansi napemphera,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapita patsogolo pangʼono patali ngati kuponya mwala, anagwada napephera kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapatukana nao kutalika kwace ngan kuponya mwala, nagwada pansi napemphera,