Luke 22:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ophunzira amene anali pafupi ndi Yesu ataona zimene zinalikudzachitika, adafunsa Yesu kuti, “Ambuye, kodi tiŵateme ndi lupanga?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene iwo akumzinga Iye anaona chimene chiti chichitike, anati, Ambuye, tidzakantha ndi lupanga kodi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Otsatira Yesu ataona zimene zimati zichitike, anati, “Ambuye, kodi timenyane ndi malupanga athu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene iwo akumzinga iye anaona cimene citi cicitike, anati, Ambuye, tidzakantha ndi lupanga kodi?