Luke 22:53 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku ndi tsiku ndidaali nanu m'Nyumba ya Mulungu, inuyo osandigwira. Koma ino ndi nthaŵi yanu ndiponso ya mphamvu za mdima.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku onse, pamene ndinali ndi inu m'Kachisi, simunatansa manja anu kundigwira: koma nyengo yino ndi yanu, ndipo ulamuliro wa mdima ndi wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lililonse ndinali nanu mʼmabwalo a mʼNyumba ya Mulungu ndipo inu simunandigwire. Koma iyi ndi nthawi yanu pamene mdima ukulamulira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku onse, pamene ndinali ndi inu m'Kacisi, simunatansa manja anu kundigwira: koma 6 nyengo yino ndi yanu, ndipo ulamuliro wa mdima ndi wanu.