Luke 22:57 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Petro adakana, adati, “Mai iwe, sindimdziŵa ameneyu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anakana, nati, Mkaziwe, sindimdziwa Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Petro anakana nati, “Mtsikana, ine sindimudziwa ameneyu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anakana, nati, Mkaziwe, sindimdziwa iye.