Luke 22:58 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita kanthaŵi pang'ono, munthu wina pomuwona adati, “Akulu inu, ndinunso mmodzi mwa iwo aja.” Koma Petro adati, “Munthu iwe, ai ndithu sindine.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo popita kamphindi, anamuona wina, nati, Iwenso uli mmodzi wa awo. Koma Petro anati, Munthu iwe, sindine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patatha kanthawi pangʼono, wina wake anamuona ndipo anati, “Iwenso ndiwe mmodzi mwa iwo.” Petro anayankha kuti, “Munthu iwe, ayi sindine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo 9 popita kamphindi, anamuona wina, nati, Iwenso uli mmodzi wa awo. Koma Petro anati, Munthu iwe, sindine.