Luke 22:59 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita ngati ora limodzi, munthu winanso adanenetsa kuti, “Ndithudi akulu aŵanso anali naye, pakuti ndi a ku Galileya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo patapita ngati ora limodzi, wina ananenetsa, kuti, Zoonadi, munthu uyunso anali naye, pakuti ndiye Mgalileya
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patatha pafupifupi ora limodzi, munthu winanso anati, “Zoonadi, munthu uyu anali ndi Iye, pakuti ndi mu Galileya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo 10 patapita ngati ora limodzi, wina ananenetsa, kuti, Zoonadi, munthu uyunso anali naye, pakuti ndiye Mgalileya.