Luke 22:69 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kuyambira tsopano Mwana wa Munthune ndidzakhala ku dzanja lamanja la Mulungu wamphamvuzonse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kuyambira tsopano Mwana wa Munthu adzakhala pa dzanja lamanja la mphamvu ya Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kuyambira tsopano, Mwana wa Munthu adzakhala ku dzanja lamanja la Mulungu wamphamvu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma 15 kuyambira tsopano Mwana wa munthu adzakhala pa dzanja lamanja la mphamvu ya Mulungu.