Luke 22:70 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo onse aja adati, “Tsono ndiye kutitu ndiwe Mwana wa Mulungu, ati?” Yesu adati, “Mwanena nokha kuti ndine amene.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo onse anati, Umo mtero, muli Mwana wa Mulungu kodi? Ndipo Iye anati kwa iwo, Munena kuti ndine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse anafunsa kuti, “Ndiye kuti ndiwe Mwana wa Mulungu?” Iye anayankha kuti, “Mwanena ndinu kuti Ndine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo onse anati, Umo mtero, muli Mwana wa Mulungu kodi? Ndipo iye anati kwa iwo, 16 Munena kuti ndine.