Luke 22:71 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo iwo aja adati, “Tikufuniranji umboni wina? Tadzimvera tokha mau akeŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo anati, Tifuniranjinso mboni? Pakuti ife tokha tinamva m'kamwa mwa Iye mwini.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo iwo anati, “Nanga tikufuniranjinso umboni wina? Ife tamva kuchokera pa milomo yake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo anati, 17 Tifuniranjinso mboni? pakuti ife tokha tinamva m'kamwa mwa iye mwini.