Luke 23:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndingomukwapula kenaka nkumumasula.” [
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndidzamkwapula ndi kummasula Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake, ine ndingomulanga, nʼkumumasula.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwacace ndidzamkwapula ndi kununasula iye. [