Luke 23:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu onse aja adayamba kufuula pamodzi kuti, “Mchotseni ameneyu, mutimasulire Barabasi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwo onse pamodzi anafuula, nati, Chotsani munthu uyu, mutimasulire Barabasi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse pamodzi anafuwula kuti, “Muchotseni munthuyu! Timasulireni Baraba!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwo onse pamodzi anapfuula, nati, Cotsani munthu uyu, mutimasulire Baraba;