Luke 23:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti masiku akubwera pamene anthu azidzati, ‘Ngodala azimai ouma, azimai osabala, azimai amene sadayamwitseko mwana.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa taonani masiku alinkudza, pamene adzati, Odala ali ouma ndi mimba yosabala, ndi mawere osayamwitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti nthawi idzabwera imene inu mudzati, ‘Ndi odala amayi osabereka, mimba zimene sizinabereke ndi mawere amene sanayamwitse!’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa taonani masiku alinkudza, pamene adzati, Odala ali ouma ndi mimba yosabala, ndi mawere osayamwitsa.