Luke 23:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ngati mtengo wauŵisi auchita zimenezi, nanga mtengo wouma ndiye adzauchita zotani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ngati azichitira izi mtengo wauwisi, nanga kudzatani ndi wouma?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa ngati anthu akuchita izi pa mtengo wauwisi, chidzachitike nʼchiyani ndi wowuma?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ngati azicitira izi mtengo wauwisi, nanga kudzatani ndi wouma?