Luke 23:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
dzuŵa litangoti bii kuda. Pamenepo chinsalu chochinga chija cha m'Nyumba ya Mulungu chidang'ambika pakatimpakati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo nsalu yotchinga ya m'Kachisi inang'ambika pakati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti dzuwa linaleka kuwala. Ndipo chinsalu cha mʼNyumba ya Mulungu chinangʼambika pakati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo nsaru yocinga ya m'Kacisi inang'ambika pakati.