Luke 23:53 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adautsitsa naukulunga m'nsalu yoyera yabafuta, nkuuika m'manda. Mandawo anali asanaikemo munthu wina aliyense.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anautsitsa, naukulunga m'nsalu yabafuta, nauika m'manda osemedwa m'mwala, m'menemo sanaike munthu ndi kale lonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anawutsitsa, nawukulunga nsalu yabafuta nawuyika mʼmanda wosemedwa mʼmwala, amene panalibe wina amene anayikidwamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo 4 anautsitsa, naukulunga m'nsaru yabafuta, nauika m'manda osemedwa m'mwala, m'menemo sanaika munthu ndi kale lonse.