Luke 24:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankakambirana za zonse zimene zidaachitika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwowa anakambirana nkhani za izi zonse zidachitika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo ankayankhulana za zonse zimene zinachitikazo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwowa anakambirana nkhani za izi zonse zidacitika.