Luke 24:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapeza chimwala chija chili chogubuduza kale kuchoka pakhomo pa manda aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapeza mwala unakunkhunizidwa kuuchotsa pamanda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anaona mwala wa pa manda utagubuduzika
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapeza mwala unakunkhunizidwa kuucotsa pamanda.