Luke 24:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso azimai ena a m'gulu lathu anatidabwitsa. Iwowo anapita ku manda m'mamaŵa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komatu akazi enanso a mwa ife anatidabwitsa, ndiwo amene analawirira kumanda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuwonjezanso apo, ena mwa amayi athu atidabwitsa ife. Iwo anapita ku manda mmamawa
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komatu akazi enanso a mwa ife anatidabwitsa, ndiwo amene analawirira kumanda;