Luke 24:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atayandikira kumudzi kumene ankapita, Yesu adachita ngati akupitirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayandikira kumudzi umene analikupitako; ndipo anachita ngati anafuna kupitirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atayandikira mudzi omwe amapitako, Yesu anachita ngati akupitirira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayandikira ku mudzi umene analikupitako; ndipo anacita ngati anafuna kupitirira.