Luke 24:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yomweyo maso ao adatsekuka, namuzindikira, Iye nkuzimirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo maso ao anatseguka, ndipo anamzindikira Iye; ndipo anawakanganukira Iye, nawachokera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka maso awo anatsekuka ndipo anamuzindikira Iye, ndipo anachoka pakati pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo maso ao anatseguka, ndipo anamzindikira iye; ndipo anawakanganukira iye, nawacokera.