Luke 24:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atanena zimenezi adaŵaonetsa manja ake ndi mapazi ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene ananena ichi, anawaonetsera iwo manja ake ndi mapazi ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye atanena izi anawaonetsa manja ake ndi mapazi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene ananena ici, anawaonetsera iwo manja ace ndi mapazi ace.